Yobu 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho Yehova anauza Satana kuti: “Chabwino, chilichonse chimene ali nacho chikhale m’manja mwako. Koma iyeyo usam’tambasulire dzanja lako ndi kum’khudza.” Pamenepo Satana anachoka pamaso pa Yehova.+
12 Choncho Yehova anauza Satana kuti: “Chabwino, chilichonse chimene ali nacho chikhale m’manja mwako. Koma iyeyo usam’tambasulire dzanja lako ndi kum’khudza.” Pamenepo Satana anachoka pamaso pa Yehova.+