Yobu 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno kunabwera Asabeya+ omwe alanda ziwetozo n’kupha abusa ake ndi lupanga. Ine ndekha ndi amene ndapulumuka kuti ndidzakuuzeni.”+
15 Ndiyeno kunabwera Asabeya+ omwe alanda ziwetozo n’kupha abusa ake ndi lupanga. Ine ndekha ndi amene ndapulumuka kuti ndidzakuuzeni.”+