Yobu 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako kunabwera chimphepo+ kuchokera kudera la kuchipululu chomwe chinawomba makona anayi a nyumbayo, ndipo nyumbayo yagwera anawo n’kuwapha. Ine ndekha ndi amene ndapulumuka kuti ndidzakuuzeni.”
19 Kenako kunabwera chimphepo+ kuchokera kudera la kuchipululu chomwe chinawomba makona anayi a nyumbayo, ndipo nyumbayo yagwera anawo n’kuwapha. Ine ndekha ndi amene ndapulumuka kuti ndidzakuuzeni.”