Yobu 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 n’kuyamba kunena kuti:“Ndinatuluka m’mimba mwa mayi anga ndili wamaliseche,+Ndipo ndidzabwerera mmenemo ndilinso wamaliseche.+Yehova wapereka,+ ndipo Yehova yemweyo watenga.+Dzina la Yehova lipitirize kutamandidwa.”+ Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:21 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo, Nsanja ya Olonda,8/15/2006, tsa. 223/15/2006, tsa. 14
21 n’kuyamba kunena kuti:“Ndinatuluka m’mimba mwa mayi anga ndili wamaliseche,+Ndipo ndidzabwerera mmenemo ndilinso wamaliseche.+Yehova wapereka,+ ndipo Yehova yemweyo watenga.+Dzina la Yehova lipitirize kutamandidwa.”+