Yobu 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye adzauluka ngati loto, ndipo sadzam’peza.Adzathamangitsidwa ngati masomphenya a usiku.+