Yobu 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mafupa ake anali odzaza ndi mphamvu zake zaunyamata,Koma adzagona nazo limodzi m’fumbi.+