Yobu 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mulungu atumize mkwiyo wake woyaka moto pa iye,N’kuudzaza m’mimba mwake.+Auvumbitsire pa iye kuti ufike mpaka m’matumbo mwake.
23 Mulungu atumize mkwiyo wake woyaka moto pa iye,N’kuudzaza m’mimba mwake.+Auvumbitsire pa iye kuti ufike mpaka m’matumbo mwake.