Yobu 20:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kumwamba kudzaulula cholakwa chake,+Ndipo dziko lapansi lidzamuukira.