Yobu 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nyumba zawo zili pa mtendere, zosaopa chilichonse,+Ndipo ndodo ya Mulungu sili pa iwo.