Yobu 30:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwo amakhala m’malo otsetsereka a m’zigwa,*M’maenje a m’nthaka ndi m’matanthwe.