-
Yobu 30:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Zoopsa zadzidzidzi zandibwerera.
Ulemerero wanga wachoka ngati kuti wauluzika ndi mphepo,
Ndipo chipulumutso changa chapita ngati mtambo.
-