Yobu 30:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Usiku mafupa anga+ amabooledwa n’kugwa pansi.Zowawa zonditafuna sizipuma.+