Yobu 30:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndimafuulira kwa inu kuti mundithandize, koma simundiyankha.+Choncho ndaimirira kuti mundimvere.