Yobu 30:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndinayendayenda mwachisoni+ pamene kunalibe kuwala.Ndinaimirira mumpingo, ndipo ndinkangofuula popempha thandizo.
28 Ndinayendayenda mwachisoni+ pamene kunalibe kuwala.Ndinaimirira mumpingo, ndipo ndinkangofuula popempha thandizo.