Yobu 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zonena zanga zikusonyeza kuwongoka kwa mtima wanga,+Ndipo milomo yanga imanena nzeru moona mtima.+ Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 33:3 Nsanja ya Olonda,11/1/1986, tsa. 17