-
Yobu 38:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Kodi ungatulutse gulu la nyenyezi la Mazaroti pa nthawi yake?
Ndipo kodi ungatsogolere gulu la nyenyezi la Asi pamodzi ndi ana ake?
-