Yobu 39:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 “Kodi ukudziwa nthawi yoikidwiratu imene mbuzi za m’mapiri zokhala m’matanthwe zimabereka?+Kodi unaona nthawi imene mphoyo zimabereka+ ndi zowawa za pobereka? Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 39:1 Nsanja ya Olonda,7/15/1997, tsa. 24
39 “Kodi ukudziwa nthawi yoikidwiratu imene mbuzi za m’mapiri zokhala m’matanthwe zimabereka?+Kodi unaona nthawi imene mphoyo zimabereka+ ndi zowawa za pobereka?