Salimo 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu inu mumanyazitsa malangizo a munthu wosautsika,Chifukwa Yehova ndiye pothawirapo pake.+