Salimo 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu Yehova, ndani amene angakhale mlendo m’chihema chanu?+Ndani angakhale m’phiri lanu lopatulika?+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:1 Nsanja ya Olonda,2/15/2014, tsa. 238/1/2003, tsa. 139/15/1989, tsa. 26
15 Inu Yehova, ndani amene angakhale mlendo m’chihema chanu?+Ndani angakhale m’phiri lanu lopatulika?+