Salimo 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Imvani dandaulo lolungama, inu Yehova. Mvetserani kulira kwanga kochonderera.+Tcherani khutu ku pemphero langa limene likutuluka pamilomo yopanda chinyengo.+
17 Imvani dandaulo lolungama, inu Yehova. Mvetserani kulira kwanga kochonderera.+Tcherani khutu ku pemphero langa limene likutuluka pamilomo yopanda chinyengo.+