Salimo 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndithudi, ubwino ndi kukoma mtima kosatha zidzanditsata masiku onse a moyo wanga.+Ndipo ine ndidzakhala m’nyumba ya Yehova mpaka kalekale.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:6 Nsanja ya Olonda,11/1/2005, tsa. 207/1/1988, tsa. 27
6 Ndithudi, ubwino ndi kukoma mtima kosatha zidzanditsata masiku onse a moyo wanga.+Ndipo ine ndidzakhala m’nyumba ya Yehova mpaka kalekale.+