Salimo 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndithudi, palibe aliyense amene adzachita manyazi mwa anthu amene chiyembekezo chawo chili mwa inu.+Amene adzachite manyazi ndi amene akuchita zinthu mwachinyengo koma osaphula kanthu.+
3 Ndithudi, palibe aliyense amene adzachita manyazi mwa anthu amene chiyembekezo chawo chili mwa inu.+Amene adzachite manyazi ndi amene akuchita zinthu mwachinyengo koma osaphula kanthu.+