Salimo 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tetezani moyo wanga ndi kundilanditsa.+Musalole kuti ndichite manyazi, pakuti ndathawira kwa inu.+
20 Tetezani moyo wanga ndi kundilanditsa.+Musalole kuti ndichite manyazi, pakuti ndathawira kwa inu.+