Salimo 27:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Yehova, imvani mawu anga pamene ndikuitana.+Ndikomereni mtima ndi kundiyankha.+