Salimo 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndilangizeni, inu Yehova, kuti ndiyende m’njira yanu.+Nditsogolereni m’njira yowongoka kuti nditetezeke kwa adani anga. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:11 Nsanja ya Olonda,7/15/2012, tsa. 26
11 Ndilangizeni, inu Yehova, kuti ndiyende m’njira yanu.+Nditsogolereni m’njira yowongoka kuti nditetezeke kwa adani anga.