Salimo 29:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye akuichititsa kudumphadumpha ngati mwana wa ng’ombe,+Lebanoni ndi Sirioni+ akudumphadumpha ngati ana a ng’ombe zakutchire. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:6 Nsanja ya Olonda,8/15/1986, tsa. 9
6 Iye akuichititsa kudumphadumpha ngati mwana wa ng’ombe,+Lebanoni ndi Sirioni+ akudumphadumpha ngati ana a ng’ombe zakutchire.