Salimo 30:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Imbani nyimbo zotamanda Yehova, inu okhulupirika ake,+Yamikani dzina lake loyera.*+