Salimo 31:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mudzawabisa m’malo otetezeka pafupi ndi inu,+Kuwachotsa pamaso pa anthu amene asonkhana pamodzi kuti awachitire chiwembu.+Mudzawabisa mumsasa wanu kwa anthu ofuna kukangana nawo.+
20 Mudzawabisa m’malo otetezeka pafupi ndi inu,+Kuwachotsa pamaso pa anthu amene asonkhana pamodzi kuti awachitire chiwembu.+Mudzawabisa mumsasa wanu kwa anthu ofuna kukangana nawo.+