Salimo 31:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma ine nditapanikizika ndinati:+“Ndidzafafanizidwa kuchoka pamaso panu.”+Ndithudi mwamva kuchonderera kwanga pamene ndinali kufuulira kwa inu kupempha thandizo.+
22 Koma ine nditapanikizika ndinati:+“Ndidzafafanizidwa kuchoka pamaso panu.”+Ndithudi mwamva kuchonderera kwanga pamene ndinali kufuulira kwa inu kupempha thandizo.+