Salimo 35:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Akhale ngati mankhusu ouluzika ndi mphepo,+Mngelo wa Yehova awapitikitse.+