Salimo 35:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Amatsegula kwambiri pakamwa pawo kuti atsutsane nane.+Iwo amati: “Eya! Eya! Tadzionera tokha.”+