Salimo 36:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Yehova, kukoma mtima kwanu kosatha kuli kumwamba.+Kukhulupirika kwanu kwafika m’mitambo.+