Salimo 36:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inu Mulungu, chilungamo chanu chili ngati mapiri anu.+Chiweruzo chanu ndi chozama kwambiri ngati madzi akuya.+Inu Yehova, mumapulumutsa munthu ndiponso nyama.+
6 Inu Mulungu, chilungamo chanu chili ngati mapiri anu.+Chiweruzo chanu ndi chozama kwambiri ngati madzi akuya.+Inu Yehova, mumapulumutsa munthu ndiponso nyama.+