Salimo 36:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Onani, ochita zinthu zopweteka anzawo agwa.+Awakanikizira pansi ndipo sakuthanso kudzuka.+