Salimo 38:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti ndinali kulankhula za cholakwa changa.+Ndipo ndinali kudera nkhawa za tchimo langa.+