Salimo 40:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma ine ndasautsika ndipo ndasauka.+Yehova amandiwerengera.+Inu ndinu thandizo langa ndi Wopereka chipulumutso kwa ine.+Inu Mulungu wanga musachedwe.+
17 Koma ine ndasautsika ndipo ndasauka.+Yehova amandiwerengera.+Inu ndinu thandizo langa ndi Wopereka chipulumutso kwa ine.+Inu Mulungu wanga musachedwe.+