Salimo 42:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Monga mmene mbawala yaikazi imalakalakira mitsinje ya madzi,Moyo wanganso ukulakalaka inu Mulungu wanga.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 42:1 Nsanja ya Olonda,6/1/2006, tsa. 91/15/1995, tsa. 1910/15/1986, tsa. 29
42 Monga mmene mbawala yaikazi imalakalakira mitsinje ya madzi,Moyo wanganso ukulakalaka inu Mulungu wanga.+