Salimo 44:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti sindinadalire uta wanga,+Ndipo si lupanga langa limene linandipulumutsa.+