Salimo 44:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndinu amene munatipulumutsa kwa adani athu,+Ndipo munanyazitsa anthu amene amadana nafe kwambiri.+