Salimo 44:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Zonsezi ndi zimene zatigwera, koma sitinakuiwaleni,+Sitinachite mwachinyengo ndi pangano lanu.+