Salimo 50:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nthawi zonse ukaona wakuba unali kusangalala naye.+Ndipo unali kugwirizana ndi anthu achigololo.+