Salimo 52:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Umakonda kwambiri zinthu zoipa kuposa zabwino,+Umakonda kwambiri kulankhula chinyengo kuposa kulankhula chilungamo.+ [Seʹlah.] Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 52:3 Nsanja ya Olonda,11/1/1989, tsa. 12
3 Umakonda kwambiri zinthu zoipa kuposa zabwino,+Umakonda kwambiri kulankhula chinyengo kuposa kulankhula chilungamo.+ [Seʹlah.]