Salimo 62:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chipulumutso ndi ulemerero wanga zili mwa Mulungu.+Iye ndi thanthwe langa lolimba ndi malo anga othawirako.+
7 Chipulumutso ndi ulemerero wanga zili mwa Mulungu.+Iye ndi thanthwe langa lolimba ndi malo anga othawirako.+