Salimo 62:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Musadalire chizolowezi chobera ena mwachinyengo,+Ndipo musakhale wachabechabe chifukwa chochita uchifwamba.+Ngati chuma chanu chachuluka, mtima wanu wonse usakhale pachumacho.+
10 Musadalire chizolowezi chobera ena mwachinyengo,+Ndipo musakhale wachabechabe chifukwa chochita uchifwamba.+Ngati chuma chanu chachuluka, mtima wanu wonse usakhale pachumacho.+