Salimo 64:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 Inu Mulungu, imvani mawu ofotokoza nkhawa zanga.+Tetezani moyo wanga kuti usaope mdani.+