Salimo 65:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu mwatembenukira dziko lapansi kuti mulipatse zinthu zochuluka,+Mwalilemeretsa kwambiri.Mtsinje wochokera kwa Mulungu ndi wosefukira ndi madzi.+Munalinganiza zinthu, kuti mbewu zawo zibale.+Umu ndi mmene mumaperekera zinthu padziko lapansi.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 65:9 Chisungiko cha Padziko Lonse, tsa. 175
9 Inu mwatembenukira dziko lapansi kuti mulipatse zinthu zochuluka,+Mwalilemeretsa kwambiri.Mtsinje wochokera kwa Mulungu ndi wosefukira ndi madzi.+Munalinganiza zinthu, kuti mbewu zawo zibale.+Umu ndi mmene mumaperekera zinthu padziko lapansi.+