Salimo 66:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwatilowetsa mu ukonde wosakira nyama,+Mwatinyamulitsa katundu wolemera m’chiuno mwathu.