Salimo 66:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndidzapereka kwa inu nsembe zathunthu zopsereza za nyama zonenepa,+Pamodzi ndi nsembe zautsi wa nkhosa zamphongo.Ndidzapereka ng’ombe yamphongo pamodzi ndi mbuzi zamphongo.+ [Seʹlah.]
15 Ndidzapereka kwa inu nsembe zathunthu zopsereza za nyama zonenepa,+Pamodzi ndi nsembe zautsi wa nkhosa zamphongo.Ndidzapereka ng’ombe yamphongo pamodzi ndi mbuzi zamphongo.+ [Seʹlah.]