Salimo 69:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Anthu ofatsa adzaona zimenezi ndipo adzakondwera.+Inu amene mukutumikira Mulungu, mtima wanu ukhalenso ndi moyo.+
32 Anthu ofatsa adzaona zimenezi ndipo adzakondwera.+Inu amene mukutumikira Mulungu, mtima wanu ukhalenso ndi moyo.+