Salimo 73:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Haa! M’kanthawi kochepa, iwo akhala chinthu chodabwitsa.+Afika pamapeto awo ndipo atha chifukwa cha masoka owagwera modzidzimutsa! Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 73:19 Nsanja ya Olonda,7/15/1993, ptsa. 29-30
19 Haa! M’kanthawi kochepa, iwo akhala chinthu chodabwitsa.+Afika pamapeto awo ndipo atha chifukwa cha masoka owagwera modzidzimutsa!